Deuteronomo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Asachulukitsenso akazi kuti mtima wake ungapatuke,+ ndipo asachulukitsenso kwambiri siliva ndi golide wake.+ 2 Samueli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake, Davide anatenganso adzakazi+ ndi akazi+ ena mu Yerusalemu atachoka ku Heburoni, moti anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. 1 Mafumu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo.
17 Asachulukitsenso akazi kuti mtima wake ungapatuke,+ ndipo asachulukitsenso kwambiri siliva ndi golide wake.+
13 Pambuyo pake, Davide anatenganso adzakazi+ ndi akazi+ ena mu Yerusalemu atachoka ku Heburoni, moti anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo.