Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 30:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 aliyense amene wakonza mtima wake+ kuti afunefune Mulungu woona Yehova, Mulungu wa makolo ake, ngakhale kuti sanadziyeretse mogwirizana ndi zinthu zopatulika.”+

  • Yesaya 55:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+

  • Amosi 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Yehova wauza anthu a m’nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yesetsani kundiyandikira,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+

  • Zefaniya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+

  • Mateyu 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena