1 Mbiri 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo analanda ziweto zawo.+ Analanda ngamila 50,000, nkhosa 250,000, abulu 2,000, ndipo anatenganso anthu 100,000.+
21 Iwo analanda ziweto zawo.+ Analanda ngamila 50,000, nkhosa 250,000, abulu 2,000, ndipo anatenganso anthu 100,000.+