Ekisodo 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Wopereka nsembe kwa milungu ina osati kwa Yehova yekha aziphedwa ndithu.+ Deuteronomo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 moti akupita kukalambira milungu ina ndi kuigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ chinthu chimene ine sindinakulamuleni,+
3 moti akupita kukalambira milungu ina ndi kuigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ chinthu chimene ine sindinakulamuleni,+