Deuteronomo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “M’bale wako, amene ndi mwana wamwamuna wa mayi ako, kapena mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, mkazi wako wokondedwa kapena bwenzi lako lapamtima,+ akayesa kukupatutsa mwamseri pokuuza kuti, ‘Tiye tikatumikire milungu ina,’+ milungu imene iwe kapena makolo ako sanaidziwe, Deuteronomo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+ Zekariya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakadzapezeka munthu aliyense wolosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka, adzamuuze kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama m’dzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulase chifukwa chakuti anali kulosera.+
6 “M’bale wako, amene ndi mwana wamwamuna wa mayi ako, kapena mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, mkazi wako wokondedwa kapena bwenzi lako lapamtima,+ akayesa kukupatutsa mwamseri pokuuza kuti, ‘Tiye tikatumikire milungu ina,’+ milungu imene iwe kapena makolo ako sanaidziwe,
9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+
3 Pakadzapezeka munthu aliyense wolosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka, adzamuuze kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama m’dzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulase chifukwa chakuti anali kulosera.+