1 Mafumu 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anayamba kubweretsa kunyumba ya Yehova zinthu zimene bambo ake anaziyeretsa, komanso zinthu zimene iyeyo anaziyeretsa. Zinthuzo zinali siliva, golide, ndi ziwiya zina.+
15 Iye anayamba kubweretsa kunyumba ya Yehova zinthu zimene bambo ake anaziyeretsa, komanso zinthu zimene iyeyo anaziyeretsa. Zinthuzo zinali siliva, golide, ndi ziwiya zina.+