1 Mafumu 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pomalizira pake Omuri anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Ahabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 1 Mafumu 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale. 1 Mafumu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo. 2 Mafumu 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu,+ chifukwa anakwatira+ mwana wa Ahabu. Choncho iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.
28 Pomalizira pake Omuri anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Ahabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.
25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.
18 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu,+ chifukwa anakwatira+ mwana wa Ahabu. Choncho iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.