1 Mafumu 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho uyu anayamba kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+ Miyambo 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zilonda zovulazidwa ndi munthu wokukonda zimakhala zokhulupirika,+ koma kuti munthu wodana nawe akupsompsone pamafunika kumuchonderera.+
20 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho uyu anayamba kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+
6 Zilonda zovulazidwa ndi munthu wokukonda zimakhala zokhulupirika,+ koma kuti munthu wodana nawe akupsompsone pamafunika kumuchonderera.+