2 Mafumu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo ankapereka ndalama zimene awerengazo kwa anthu ogwira ntchito+ amene anaikidwa panyumba ya Yehova. Anthu ogwira ntchitowo ankagwiritsa ntchito ndalamazo polipira amisiri a matabwa, omanga amene anali kugwira ntchito panyumba ya Yehovayo, 2 Mafumu 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe,+ ukamuuze kuti asonkhanitse pamodzi ndalama zonse+ zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo+ atolera kwa anthu.
11 Iwo ankapereka ndalama zimene awerengazo kwa anthu ogwira ntchito+ amene anaikidwa panyumba ya Yehova. Anthu ogwira ntchitowo ankagwiritsa ntchito ndalamazo polipira amisiri a matabwa, omanga amene anali kugwira ntchito panyumba ya Yehovayo,
4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe,+ ukamuuze kuti asonkhanitse pamodzi ndalama zonse+ zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo+ atolera kwa anthu.