Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Bisilamu, Mitiredati, Tabeeli, ndi anzake ena onse analemba kalata kwa Aritasasita mfumu ya Perisiya m’masiku a mfumuyo. Kalatayo anaimasulira m’Chiaramu n’kuilemba m’zilembo za Chiaramu.+

  • Ezara 4:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mawu amene analembedwa m’kalata ya mfumu Aritasasita atawerengedwa pamaso pa Rehumu,+ Simusai+ mlembi, ndi anzawo,+ iwo anapita msangamsanga kwa Ayuda ku Yerusalemu n’kukawaletsa ntchitoyo mwankhondo.+

  • Nehemiya 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Aluya,+ Aamoni+ ndi Aasidodi+ atamva kuti ntchito yokonza mpanda wa Yerusalemu ikupita patsogolo, pakuti malo ogumuka anali atayamba kutsekedwa, anakwiya kwambiri.

  • Nehemiya 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Komanso adani athu anali kunena kuti: “Sadzadziwa+ kapena kuona kuti tikubwera, kufikira titafika pakati pawo ndipo tidzawapha ndithu ndi kuimitsa ntchito yomangayo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena