2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+ Salimo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu munati: “Ndidzakupatsa nzeru ndi kukulangiza njira yoti uyendemo.+Ndidzakupatsa malangizo ndi kukuyang’anira.+ Salimo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani! Diso la Yehova lili pa anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha,+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+
8 Inu munati: “Ndidzakupatsa nzeru ndi kukulangiza njira yoti uyendemo.+Ndidzakupatsa malangizo ndi kukuyang’anira.+
18 Taonani! Diso la Yehova lili pa anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha,+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+