Levitiko 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Ngati akupereka nkhosa+ kapena mbuzi kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka+ mwana wamphongo wopanda chilema.+ Levitiko 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo anauza Aroni kuti: “Tenga ng’ombe yaing’ono kuti ikhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza.+ Nyama zonsezi zikhale zopanda chilema, ndipo uzipereke kwa Yehova.+
10 “‘Ngati akupereka nkhosa+ kapena mbuzi kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka+ mwana wamphongo wopanda chilema.+
2 Pamenepo anauza Aroni kuti: “Tenga ng’ombe yaing’ono kuti ikhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza.+ Nyama zonsezi zikhale zopanda chilema, ndipo uzipereke kwa Yehova.+