Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+

  • Deuteronomo 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+

  • 2 Mbiri 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndasankha+ ndi kuyeretsa nyumba ino kuti dzina langa+ likhale pamenepa mpaka kalekale,+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala pamenepa nthawi zonse.+

  • Salimo 132:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka muyaya.+

      Ndidzakhala mmenemu, pakuti ndimafunitsitsa kukhala m’malo amenewa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena