Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ndipo Yohanani anabereka Azariya.+ Iye ndiye anali wansembe m’nyumba imene Solomo anamanga ku Yerusalemu.

  • 2 Mbiri 31:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Azariya,+ wansembe wamkulu wa nyumba ya Zadoki,+ anamuyankha kuti: “Kuyambira pamene anthu anayamba kubweretsa zopereka+ m’nyumba ya Yehova, pakhala kudya ndi kukhuta+ ndipo pali zotsala zambiri,+ chifukwa Yehova wadalitsa anthu ake+ ndipo zonse mukuzionazi n’zimene zatsala.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena