1 Mafumu 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chakudya cha kunyumba yachifumu ya Solomo tsiku lililonse chinkakhala ufa wosalala wokwana miyezo 30 ya kori,*+ ufa wamba wokwana miyezo 60 ya kori, Ezekieli 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Poyeza mafuta oti muzipereka, muzigwiritsa ntchito mtsuko woyezera monga muyezo wanu wa nthawi zonse. Mtsukowo uzikwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa kori.* Mitsuko 10 izikwana homeri chifukwa mitsuko 10 imakwana homeri.
22 Chakudya cha kunyumba yachifumu ya Solomo tsiku lililonse chinkakhala ufa wosalala wokwana miyezo 30 ya kori,*+ ufa wamba wokwana miyezo 60 ya kori,
14 Poyeza mafuta oti muzipereka, muzigwiritsa ntchito mtsuko woyezera monga muyezo wanu wa nthawi zonse. Mtsukowo uzikwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa kori.* Mitsuko 10 izikwana homeri chifukwa mitsuko 10 imakwana homeri.