Ezara 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda. Yesaya 40:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pali Winawake amene amakhala pamwamba pa dziko lapansi lozungulira,+ limene okhalamo ake ali ngati ziwala. Iye anayala kumwamba ngati nsalu yopyapyala, ndipo anakutambasula ngati hema wokhalamo.+
2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda.
22 Pali Winawake amene amakhala pamwamba pa dziko lapansi lozungulira,+ limene okhalamo ake ali ngati ziwala. Iye anayala kumwamba ngati nsalu yopyapyala, ndipo anakutambasula ngati hema wokhalamo.+