Aefeso 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Osati mwachiphamaso ngati ofuna kukondweretsa anthu,+ koma monga akapolo a Khristu, ochita chifuniro cha Mulungu ndi moyo wonse.+ Akolose 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,
6 Osati mwachiphamaso ngati ofuna kukondweretsa anthu,+ koma monga akapolo a Khristu, ochita chifuniro cha Mulungu ndi moyo wonse.+
23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,