1 Mbiri 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Midzi yawo yonse yozungulira mizinda imeneyi inakafika mpaka ku Baala.+ Awa anali malo awo okhala ndi mndandanda wa mayina awo wotsatira makolo. 1 Mbiri 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli onse analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo+ m’Buku la Mafumu a Isiraeli. Ayuda anatengedwa kupita ku ukapolo+ ku Babulo chifukwa cha kusakhulupirika kwawo.
33 Midzi yawo yonse yozungulira mizinda imeneyi inakafika mpaka ku Baala.+ Awa anali malo awo okhala ndi mndandanda wa mayina awo wotsatira makolo.
9 Aisiraeli onse analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo+ m’Buku la Mafumu a Isiraeli. Ayuda anatengedwa kupita ku ukapolo+ ku Babulo chifukwa cha kusakhulupirika kwawo.