1 Mbiri 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana amene Davide+ anabereka ku Heburoni+ anali awa: woyamba Aminoni,+ wobadwa kwa Ahinowamu+ wa ku Yezereeli,+ wachiwiri Danieli, wobadwa kwa Abigayeli+ wa ku Karimeli,+
3 Ana amene Davide+ anabereka ku Heburoni+ anali awa: woyamba Aminoni,+ wobadwa kwa Ahinowamu+ wa ku Yezereeli,+ wachiwiri Danieli, wobadwa kwa Abigayeli+ wa ku Karimeli,+