Miyambo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu adzatamandidwa chifukwa cha pakamwa pake panzeru,+ koma wa mtima wopotoka adzanyozedwa.+ Yeremiya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzakupatsani abusa amene mtima wanga wakonda+ ndipo iwo adzakuthandizani kudziwa zinthu zambiri ndiponso kumvetsa bwino zinthu.+
15 Ndidzakupatsani abusa amene mtima wanga wakonda+ ndipo iwo adzakuthandizani kudziwa zinthu zambiri ndiponso kumvetsa bwino zinthu.+