Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asaipitse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, mkate wa Mulungu wawo,+ choncho azikhala oyera.+

  • Levitiko 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho muzim’patula+ chifukwa ndiye wopereka mkate wa Mulungu wanu. Azikhala woyera kwa inu,+ chifukwa ine Yehova, amene ndikukupatulani, ndine woyera.+

  • Yesaya 52:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena