Genesis 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndapalana ubwenzi ndi Abulahamu kuti aphunzitse ana ake ndi mbadwa zake kuyenda m’njira ya Yehova ndi kuchita chilungamo.+ Awaphunzitse kutero, kuti Yehova adzakwaniritse kwa Abulahamu zimene ananena zokhudza iye.”+ Salimo 112:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana ake adzakhala amphamvu padziko lapansi.+ ד [Daʹleth]Ndipo m’badwo wa anthu olungama udzadalitsidwa.+ Miyambo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+ Miyambo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wolungama amayenda ndi mtima wosagawanika,+ ndipo ana ake amakhala odala.+
19 Ndapalana ubwenzi ndi Abulahamu kuti aphunzitse ana ake ndi mbadwa zake kuyenda m’njira ya Yehova ndi kuchita chilungamo.+ Awaphunzitse kutero, kuti Yehova adzakwaniritse kwa Abulahamu zimene ananena zokhudza iye.”+
2 Ana ake adzakhala amphamvu padziko lapansi.+ ד [Daʹleth]Ndipo m’badwo wa anthu olungama udzadalitsidwa.+
22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+