Levitiko 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika. Yoswa 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+ Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu, ndipo sindinabise cholakwa changa.+Ndinati: “Ndidzaulula kwa Yehova machimo anga.”+Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ [Seʹlah.] Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika.
19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu, ndipo sindinabise cholakwa changa.+Ndinati: “Ndidzaulula kwa Yehova machimo anga.”+Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ [Seʹlah.]
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+