1 Mafumu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+ 2 Mbiri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 upatsidwa nzeru ndi luntha lodziwa zinthu.+ Ndikupatsanso katundu, chuma, ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhale,+ ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+ 2 Mbiri 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru kwambiri+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+
12 upatsidwa nzeru ndi luntha lodziwa zinthu.+ Ndikupatsanso katundu, chuma, ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhale,+ ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+
22 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru kwambiri+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.