Nehemiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sanibalati+ wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wachiamoni,+ atamva zimenezi anaipidwa kwambiri+ kuti kwabwera munthu wofunira ana a Isiraeli zabwino. Nehemiya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Sanibalati+ atangomva kuti tinali kumanganso mpanda, anakhumudwa ndi kukwiya kwambiri,+ ndipo anali kunyoza+ Ayuda. Nehemiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani+ zinthu zonse zimene Tobia+ ndi Sanibalati anachita. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi+ ndi aneneri ena onse amene anali kuyesetsabe kundiopseza.
10 Sanibalati+ wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wachiamoni,+ atamva zimenezi anaipidwa kwambiri+ kuti kwabwera munthu wofunira ana a Isiraeli zabwino.
4 Tsopano Sanibalati+ atangomva kuti tinali kumanganso mpanda, anakhumudwa ndi kukwiya kwambiri,+ ndipo anali kunyoza+ Ayuda.
14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani+ zinthu zonse zimene Tobia+ ndi Sanibalati anachita. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi+ ndi aneneri ena onse amene anali kuyesetsabe kundiopseza.