Malaki 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndakutumizirani lamulo limeneli+ kuti pangano+ limene ndinapangana ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa makamu.
4 Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndakutumizirani lamulo limeneli+ kuti pangano+ limene ndinapangana ndi Levi lipitirire,”+ watero Yehova wa makamu.