-
Nehemiya 10:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Komanso tinachita maere+ okhudza ansembe, Alevi ndi anthu oti azibweretsa nkhuni+ kunyumba ya Mulungu wathu, mogwirizana ndi nyumba ya makolo athu, pa nthawi zoikidwiratu, chaka ndi chaka kuti aziziyatsira moto paguwa lansembe la Yehova Mulungu wathu,+ malinga ndi zimene zinalembedwa m’chilamulo.+
-