Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.

  • 2 Samueli 21:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho mfumu inaitana Agibeoni+ ndi kulankhula nawo. (Agibeoni sanali ana a Isiraeli koma otsala mwa Aamori.+ Ana a Isiraeli analumbira kwa Aamori,+ koma Sauli anali kufuna kuwapha+ onse chifukwa chakuti iye anali kuchitira nsanje+ ana a Isiraeli ndi ana a Yuda.)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena