Ezara 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Akuluakuluwo anatiyankha kuti: ‘Ife ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi,+ ndipo tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga ndi kuimaliza.+ Nehemiya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Poyankha, mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?”+ Nthawi yomweyo ndinapemphera+ kwa Mulungu wakumwamba.+ Salimo 115:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+
11 “Akuluakuluwo anatiyankha kuti: ‘Ife ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi,+ ndipo tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga ndi kuimaliza.+
4 Poyankha, mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?”+ Nthawi yomweyo ndinapemphera+ kwa Mulungu wakumwamba.+