Nyimbo ya Solomo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Taonani! Ndi bedi la Solomo. Amuna 60 amphamvu ochokera mwa amuna amphamvu a Isiraeli alizungulira.+
7 “Taonani! Ndi bedi la Solomo. Amuna 60 amphamvu ochokera mwa amuna amphamvu a Isiraeli alizungulira.+