Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 55:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine ndidzafuulira Mulungu.+Ndipo Yehova adzandipulumutsa.+