Nehemiya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuwonjezera apo, ndinagwira nawo ntchito yomanga mpandawo+ ndipo sitinakhale ndi minda.+ Atumiki anga onse anasonkhana pamodzi kumeneko kuti agwire ntchito.
16 Kuwonjezera apo, ndinagwira nawo ntchito yomanga mpandawo+ ndipo sitinakhale ndi minda.+ Atumiki anga onse anasonkhana pamodzi kumeneko kuti agwire ntchito.