Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+ Afilipi 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Komanso simukuchita mantha m’njira iliyonse ndi okutsutsani.+ Kwa iwo, chimenechi ndi chizindikiro chakuti adzawonongedwa, koma kwa inu, ndi chizindikiro cha chipulumutso.+ Chizindikiro chimenechi n’chochokera kwa Mulungu.
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
28 Komanso simukuchita mantha m’njira iliyonse ndi okutsutsani.+ Kwa iwo, chimenechi ndi chizindikiro chakuti adzawonongedwa, koma kwa inu, ndi chizindikiro cha chipulumutso.+ Chizindikiro chimenechi n’chochokera kwa Mulungu.