Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 23:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anauza anthu onse kuti aimirire,+ kuyambira kumbali yakumanja ya nyumbayo mpaka kukafika kumbali yakumanzere ya nyumbayo. Anaimiriranso pafupi ndi guwa lansembe ndiponso pafupi ndi nyumbayo. Anthuwo anazungulira mfumuyo kumbali zonse, aliyense atatenga chida chake m’manja.

  • 2 Mbiri 32:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kuwonjezera apo, iye analimba mtima n’kumanga makoma onse a mpanda amene anali ogumuka.+ Anamanga nsanja+ pamwamba pa mpandawo ndipo kunja kwake anamangako mpanda wina.+ Anakonzanso Chimulu cha Dothi*+ cha mu Mzinda wa Davide ndipo anapanga zida+ zambiri ndi zishango.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena