2 Mbiri 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwonjezera apo, wansembe Yehoyada anapatsa atsogoleri a magulu a asilikali 100 aja+ mikondo, zishango ndi zishango zozungulira+ zimene zinali za Mfumu Davide,+ zomwe zinali m’nyumba ya Mulungu woona.+ 2 Mbiri 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anauza anthu onse kuti aimirire,+ kuyambira kumbali yakumanja ya nyumbayo mpaka kukafika kumbali yakumanzere ya nyumbayo. Anaimiriranso pafupi ndi guwa lansembe ndiponso pafupi ndi nyumbayo. Anthuwo anazungulira mfumuyo kumbali zonse, aliyense atatenga chida chake m’manja.
9 Kuwonjezera apo, wansembe Yehoyada anapatsa atsogoleri a magulu a asilikali 100 aja+ mikondo, zishango ndi zishango zozungulira+ zimene zinali za Mfumu Davide,+ zomwe zinali m’nyumba ya Mulungu woona.+
10 Iye anauza anthu onse kuti aimirire,+ kuyambira kumbali yakumanja ya nyumbayo mpaka kukafika kumbali yakumanzere ya nyumbayo. Anaimiriranso pafupi ndi guwa lansembe ndiponso pafupi ndi nyumbayo. Anthuwo anazungulira mfumuyo kumbali zonse, aliyense atatenga chida chake m’manja.