Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Samala kuti usalankhule mawu achabe mumtima mwako+ kuti, ‘Chaka cha 7, chaka choti anthu angongole amasuke chayandikira,’+ kuti usaolowere manja m’bale wako wosaukayo,+ osam’patsa kalikonse. Pamenepo iye adzafuulira Yehova chifukwa cha zimene iweyo wam’chitira+ ndipo udzapezeka kuti wachimwa.+

  • Miyambo 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Aliyense wotseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,+ nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+

  • Luka 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena