Genesis 47:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tiferenji ife inu mukuona,+ ndipo minda yathu ikhalirenji yogonera? Mutigule limodzi ndi minda yathu potipatsa chakudya+ kuti tikhale akapolo a Farao. Mutipatse tirigu kuti tikhale ndi moyo tisafe, kutinso minda yathu isagonere.”+
19 Tiferenji ife inu mukuona,+ ndipo minda yathu ikhalirenji yogonera? Mutigule limodzi ndi minda yathu potipatsa chakudya+ kuti tikhale akapolo a Farao. Mutipatse tirigu kuti tikhale ndi moyo tisafe, kutinso minda yathu isagonere.”+