Genesis 47:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho, Yosefe anagulira Farao nthaka yonse ya Aiguputo,+ chifukwa Mwiguputo aliyense anagulitsa munda wake. Anatero chifukwa njala inali itawapanikiza koopsa, moti nthaka yonse inakhala ya Farao.
20 Choncho, Yosefe anagulira Farao nthaka yonse ya Aiguputo,+ chifukwa Mwiguputo aliyense anagulitsa munda wake. Anatero chifukwa njala inali itawapanikiza koopsa, moti nthaka yonse inakhala ya Farao.