2 Samueli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide+ ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+
5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide+ ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+