Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Munthu akagulitsa mwana wake wamkazi kukhala kapolo,+ sadzachoka mmene akapolo aamuna amachokera.

  • Deuteronomo 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ngati anakugulitsa m’bale wako, Mheberi wamwamuna kapena wamkazi,+ ndipo wakutumikira zaka 6, m’chaka cha 7 uzim’masula ndi kumulola kuchoka.+

  • 2 Mafumu 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mayi wina yemwe anali mmodzi wa akazi a ana+ a aneneri, anafika kwa Elisa n’kulankhula mokweza kuti: “Mtumiki wanu yemwe anali mwamuna wanga anamwalira. Inu mukudziwa bwino kuti mtumiki wanuyo anali woopa+ Yehova. Tsopano kwabwera wangongole+ kudzatenga ana anga onse awiri kuti akakhale akapolo ake.”

  • Miyambo 22:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Wolemera ndi amene amalamulira anthu osauka,+ ndipo wobwereka amakhala kapolo wa wobwereketsayo.+

  • Mateyu 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma popeza kuti analibe choti apereke pobweza ngongoleyo, mbuye wake analamula kuti mwamuna ameneyu, mkazi wake, ana ake komanso zonse zimene anali nazo zigulitsidwe ndi kum’bwezera ndalama zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena