Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tili ndi ufulu wa kudya+ ndi kumwa, si choncho kodi?

  • 1 Akorinto 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma sindinagwiritse ntchito dongosolo lililonse loterolo.+ Ndiponso, sikuti ndalemba zimenezi kuti dongosolo limeneli liyambe kugwira ntchito kwa ine ayi, pakuti zingakhale bwino kuti ineyo ndife kusiyana ndi kuti . . . ndipo palibe munthu angatsutse chifukwa chimene ndikudzitamira!+

  • 2 Atesalonika 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena