Nehemiya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Onsewo anali kungofuna kutichititsa mantha, ndipo anali kunena kuti: “Manja awo+ adzalefuka ndipo adzasiya kugwira ntchitoyi, mwakuti siitha.” Inu Mulungu wanga, limbitsani manja anga.+ Nehemiya 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anamulemba ganyu+ n’cholinga choti ndichite mantha+ kuti ndikalowe m’kachisi ndi kuchimwa.+ Mwakutero, akanandiipitsira dzina langa+ kuti azindinyoza.+
9 Onsewo anali kungofuna kutichititsa mantha, ndipo anali kunena kuti: “Manja awo+ adzalefuka ndipo adzasiya kugwira ntchitoyi, mwakuti siitha.” Inu Mulungu wanga, limbitsani manja anga.+
13 Iwo anamulemba ganyu+ n’cholinga choti ndichite mantha+ kuti ndikalowe m’kachisi ndi kuchimwa.+ Mwakutero, akanandiipitsira dzina langa+ kuti azindinyoza.+