1 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu. 1 Mbiri 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa magulu a alonda a pazipatawa, ntchito ya atsogoleri awo inali yofanana ndi ya abale awo,+ ndipo inali yotumikira panyumba ya Yehova. Ezara 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a alonda a pachipata, omwe anali ana a Salumu,+ ana a Ateri,+ ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita,+ ndi ana a Sobai, onse analipo 139.
26 Tsopano awa ndiwo magulu a alonda a pazipata:+ Pa mbadwa za Kora+ panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.
12 Pa magulu a alonda a pazipatawa, ntchito ya atsogoleri awo inali yofanana ndi ya abale awo,+ ndipo inali yotumikira panyumba ya Yehova.
42 Ana a alonda a pachipata, omwe anali ana a Salumu,+ ana a Ateri,+ ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita,+ ndi ana a Sobai, onse analipo 139.