Levitiko 25:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pakuti ana a Isiraeli ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Asamadzigulitse mmene amadzigulitsira akapolo.
42 Pakuti ana a Isiraeli ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Asamadzigulitse mmene amadzigulitsira akapolo.