Deuteronomo 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo+ ndipo Yehova Mulungu wako anakutulutsa kumeneko ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula.+ N’chifukwa chake Yehova Mulungu wako anakulamula kuti uzisunga tsiku la sabata.+ Deuteronomo 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+
15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo+ ndipo Yehova Mulungu wako anakutulutsa kumeneko ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula.+ N’chifukwa chake Yehova Mulungu wako anakulamula kuti uzisunga tsiku la sabata.+
26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+