1 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno tsiku lina Elikana anali kupereka nsembe, ndipo anapereka magawo a nsembeyo kwa mkazi wake Penina ndi kwa ana ake onse aamuna ndi aakazi,+ Luka 11:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma inu, perekani zimene zili mkati monga mphatso zachifundo,+ mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera. Machitidwe 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero iwo anapitiriza kulabadira zimene atumwiwo anali kuphunzitsa. Iwo anali kugawana zinthu,+ kudya chakudya+ komanso kupemphera.+
4 Ndiyeno tsiku lina Elikana anali kupereka nsembe, ndipo anapereka magawo a nsembeyo kwa mkazi wake Penina ndi kwa ana ake onse aamuna ndi aakazi,+
41 Koma inu, perekani zimene zili mkati monga mphatso zachifundo,+ mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera.
42 Chotero iwo anapitiriza kulabadira zimene atumwiwo anali kuphunzitsa. Iwo anali kugawana zinthu,+ kudya chakudya+ komanso kupemphera.+