1 Mbiri 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu. Salimo 103:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+Chilichonse mkati mwanga, chitamande dzina lake loyera.+
20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu.