1 Mafumu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mikaya anapitiriza kunena kuti: “Choncho imvani mawu a Yehova:+ Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu,+ makamu onse akumwamba ataimirira kudzanja lake lamanja ndi kumanzere kwake.+ Salimo 103:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tamandani Yehova inu makamu ake onse,+Inu atumiki ake onse ochita chifuniro chake.+
19 Mikaya anapitiriza kunena kuti: “Choncho imvani mawu a Yehova:+ Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu,+ makamu onse akumwamba ataimirira kudzanja lake lamanja ndi kumanzere kwake.+