Ezara 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 inu mfumu dziwani kuti Ayuda amene anachokera kwa inu n’kudzatipeza kuno, ali ku Yerusalemu. Iwo akumanga mzinda woukira ndi woipa uja, ndipo akumanga mpanda+ ndi kukonzanso maziko ake. Ezara 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakalowerere ntchito yomanga nyumba ya Mulunguyo.+ Bwanamkubwa wa Ayuda ndi akulu a Ayuda amanganso nyumba ya Mulunguyo pamalo ake.
12 inu mfumu dziwani kuti Ayuda amene anachokera kwa inu n’kudzatipeza kuno, ali ku Yerusalemu. Iwo akumanga mzinda woukira ndi woipa uja, ndipo akumanga mpanda+ ndi kukonzanso maziko ake.
7 Musakalowerere ntchito yomanga nyumba ya Mulunguyo.+ Bwanamkubwa wa Ayuda ndi akulu a Ayuda amanganso nyumba ya Mulunguyo pamalo ake.