Ezara 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ana a Harimu,+ 1,017. Ezara 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa ana a Harimu+ panali Maaseya, Eliya, Semaya, Yehiela ndi Uziya. Nehemiya 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Woimira nyumba ya Harimu+ anali Adena, woimira nyumba ya Merayoti anali Helikai.